October 30–November 5 YOBU 11-12 YAMBANI October 30–November 5 Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero Mawu Oyamba (1 min.) CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Njira Zitatu Zomwe Tingapezere Nzeru N’kumazigwiritsa Ntchito”: (10 min.) Mfundo Zothandiza: (10 min.) Yob 12:11—Kodi mfundo ya palembali ingatithandize bwanji kuti tizimvetsera bwino ena akamalankhula? (w08-CN 8/1 11:5) Yankho Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina? Yankho Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 12:1-13 (th phunziro 5) KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu, ndipo musiyireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 1) Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni ku misonkhano yathu, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 13) Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 12 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 19) MOYO WATHU WACHIKHRISTU Nyimbo Na. 135 “Makolo, Muzithandiza Ana Anu Kupeza Nzeru Zochokera kwa Mulungu”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo. Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 55:1-4 Mawu Omaliza (3 min.) Nyimbo Na. 92 ndi Pemphero Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena October 30–November 5 UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 30–November 5, 2023 Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya October 30–November 5, 2023 https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023342/univ/art/202023342_univ_sqr_xl.jpg mwb23.9 23