CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Njira Zitatu Zomwe Tingapezere Nzeru N’kumazigwiritsa Ntchito

Njira Zitatu Zomwe Tingapezere Nzeru N’kumazigwiritsa Ntchito

Muzichita chidwi ndi zinthu zam’chilengedwe (Yob 12:​7-9; w09-CN 4/15 6:17)

Muzikhala pa ubwenzi ndi Akhristu okhulupirika (Yob 12:12; w21.06 23:10-12)

Muziphunzira mfundo za Mulungu ndipo muzizigwiritsa ntchito pa moyo wanu (Yob 12:16; it-2 1190:2)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndaphunzira chiyani chifukwa chocheza ndi Akhristu okhulupirika?