October 9-15

YOBU 4-5

October 9-15
  • Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Samalani ndi Nkhani Zabodza”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yob 4:4—Kodi Yobu anapereka chitsanzo chabwino chiti kwa Akhristu masiku ano? (w03-CN 5/15 22:5-6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 5:​1-12 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 78

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 52

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero