CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Samalani ndi Nkhani Zabodza

Samalani ndi Nkhani Zabodza

Zimene Elifazi ankanena zinkaoneka ngati zoona chifukwa anali wamkulu komanso wanzeru (Yob 4:1; it-1 713:11)

Ziwanda zinamutsogolera kuti akapereke uthenga wofooketsa kwa Yobu (Yob 4:​14-16; w05-CN 9/15 26:2)

Zina mwa zomwe Elifazi ananena zinali zoona, koma anazigwiritsa ntchito molakwika (Yob 4:19; w10-CN 2/15 19:5-6)

Dziko la Satanali limafalitsa nkhani zabodza zowononga.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimapeza nthawi yoti nditsimikizire kaye ngati nkhani zimene ndikumva kapena kuwerenga zilidi zoona?’—mrt 32 ¶13-17