September 11-17

ESITERE 3-5

September 11-17

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 65

  • Khalani Bwenzi la Yehova—Nditsanzire Esitere: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka funsani ana omwe munawasankhiratu funso ili: Kodi mungatsanzire bwanji kulimba mtima kwa Esitere?

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff 49:6, Komanso zomwe taphunzira, kubwereza ndi zolinga

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 130 ndi Pemphero