CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri YAMBANI Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Moredekai anapereka chitsanzo chabwino cha kukhala wolimba mtima komanso wokhulupirika kwa Yehova (Est 3:2-4; it-2 431:7) Anathandiza Esitere kuona kuti akhoza kuchita zabwino (Est 4:7, 8; it-2 431:9) Analimbikitsa Esitere kuti akhale wolimba mtima komanso azidalira Yehova (Est 4:12-14; ia 16:22-23) DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zolankhula komanso zochita zanga zimathandiza ena mumpingo kuti azichita zambiri potumikira Yehova?’ Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri Chinenero Chamanja cha ku Malawi Muzithandiza Ena Kuti Azichita Zambiri https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023324/sign/art/202023324_sign_sqr_xl.jpg mwb23.9 5