September 18-24 ESITERE 6-8 YAMBANI September 18-24 Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero Mawu Oyamba (1 min.) CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino”: (10 min.) Mfundo Zothandiza: (10 min.) Est 7:4—Kodi kuwonongedwa kwa Ayuda kukanawonongetsa bwanji ‘zinthu zambiri za mfumu’? (w06-CN 3/1 11:1) Yankho Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina? Yankho Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Est 8:9-17 (th phunziro 5) KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3) Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 12) Nkhani: (5 min.) w22.01 2:8-10—Mutu: Tiziphunzitsa Mogwira Mtima Ngati Yakobo—Uthenga Wathu Uzikhala Wosavuta Kumva. (th phunziro 17) MOYO WATHU WACHIKHRISTU Nyimbo Na. 148 “Muzidalira Yehova Anzanu Akamakuvutitsani”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo. Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 50:1-5, Komanso Video yakuti Tetezani Ana Anu Mawu Omaliza (3 min.) Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena September 18-24 UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya September 18-24, 2023 Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya September 18-24, 2023 https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023325/univ/art/202023325_univ_sqr_xl.jpg mwb23.9 6