September 25–October 1 ESITERE 9-10 YAMBANI September 25–October 1 Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero Mawu Oyamba (1 min.) CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena”: (10 min.) Mfundo Zothandiza: (10 min.) Est 9:15, 16—N’chifukwa chiyani Ayuda sanatenge zofunkha? (w06-CN 3/1 11:4) Yankho Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina? Yankho Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Est 9:1-10 (th phunziro 11) KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 6) Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 13) Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 12 mawu oyamba a pa Fufuzani Mozama ndi mfundo 4 (th phunziro 19) MOYO WATHU WACHIKHRISTU Nyimbo Na. 117 “Abusa Amene Amachitira Zabwino Anthu a Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo. Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 50:6-7, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga Mawu Omaliza (3 min.) Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena September 25–October 1 UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU–NDANDANDA YA MISONKHANO Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya September 25–October 1, 2023 Chinenero Chamanja cha ku Malawi Ndandanda ya Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya September 25–October 1, 2023 https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/202023328/univ/art/202023328_univ_sqr_xl.jpg mwb23.9 9