CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena

Anagwiritsa Ntchito Udindo Wake Pothandiza Anthu Ena

Moredekai anapatsidwa udindo waukulu kwambiri (Est 9:4; it-2 432:2)

Iye anayambitsa chikondwerero cha chaka ndi chaka pofuna kulemekeza Yehova (Est 9:​20-22, 26-28; it-2 716:5)

Iye ankachitira zabwino anthu a Mulungu (Est 10:3)

Masiku ano, anthu amene ali ndi udindo m’gulu la Yehova amayesetsa kutsanzira chitsanzo cha Moredekai.—cl-CN 101-102:12-13.