Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni kabuku kakuti, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 1)
Nkhani: (5 min.) w20.11 12-14 ¶3-7—Mutu: Anathandizidwa ndi Yesu Komanso Angelo. (th phunziro 14)