Mupeze Mayankho a Mafunso Awa YAMBANI Mupeze Mayankho a Mafunso Awa Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu 1. Kodi tingadziwe bwanji anthu okonda mtendere? (Luka 10:6) 2. Kodi tingathandize bwanji anthu okonda mtendere kuti akhale mabwenzi a Mulungu? (Mat. 10:11) 3. Kodi Kalonga Wamtendere amatithandiza bwanji kupeza anthu okonda mtendere? (Yes. 9:6, 7; Mat. 28:20) 4. Kodi tingasonyeze bwanji kuti ndife anthu okonda mtendere? (Sal. 11:5; 2 Tim. 2:24; Yak. 3:17, 18) 5. Kodi anthu okonda mtendere amathandizana bwanji? (2 Akor. 6:13) 6. Kodi tingatani kuti ‘tipitirize kugonjetsa choipa mwa kuchita chabwino’? (Aroma 12:2, 6, 10, 18) © 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania CA-brpgm23-CN Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mupeze Mayankho a Mafunso Awa PULOGALAMU YA MSONKHANO WADERA WOKHALA NDI WOIMIRA NTHAMBI WA 2022-2023 Mupeze Mayankho a Mafunso Awa Chinenero Chamanja cha ku Malawi Mupeze Mayankho a Mafunso Awa https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png CA-brpgm23 p. 4