Lachisanu YAMBANI Lachisanu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu “Chikondi n’choleza mtima” 1 Akorinto 13:4 M’Mawa 9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo 9:30 Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero 9:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: N’chifukwa Chiyani Tiyenera ‘Kukhala Oleza Mtima’? (Yakobo 5:7, 8; Akolose 1:9-11; 3:12) 10:10 NKHANI YOSIYIRANA: “Chilichonse Chili ndi Nthawi Yake” • Muziganizira Mmene Yehova Amaonera Nthawi (Mlaliki 3:1-8, 11) • Kulimbitsa Ubwenzi ndi Anzathu Kumatenga Nthawi (Miyambo 17:17) • Kukula Mwauzimu Kumatenga Nthawi (Maliko 4:26-29) • Kukwaniritsa Zolinga Kumatenga Nthawi (Mlaliki 11:4, 6) 11:05 Nyimbo Na. 143 ndi Zilengezo 11:15 KUWERENGA BAIBULO MWASEWERO: Davide Anayembekezera Yehova (1 Samueli 24:2-15; 25:1-35; 26:2-12; Salimo 37:1-7) 11:45 Muzisangalala ndi Kuleza Mtima kwa Mulungu (Aroma 2:4, 6, 7; 2 Petulo 3:8, 9; Chivumbulutso 11:18) 12:15 Nyimbo Na. 147 ndi Kupuma Masana 1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo 1:45 Nyimbo Na. 17 1:50 Muzitsanzira Kuleza Mtima kwa Yesu (Aheberi 12:2, 3) 2:10 NKHANI YOSIYIRANA: Muzitsanzira Anthu Amene Anadalitsidwa Chifukwa cha Kuleza Mtima • Abulahamu ndi Sara (Aheberi 6:12) • Yosefe (Genesis 39:7-9) • Yobu (Yakobo 5:11) • Moredekai ndi Esitere (Esitere 4:11-16) • Zekariya ndi Elizabeti (Luka 1:6, 7) • Paulo (Machitidwe 14:21, 22) 3:10 Nyimbo Na. 11 ndi Zilengezo 3:20 NKHANI YOSIYIRANA: Zimene Chilengedwe Chimatiphunzitsa Zokhudza Mmene Yehova Amaonera Nthawi • Zomera (Mateyu 24:32, 33) • Zolengedwa za M’madzi (2 Akorinto 6:2) • Mbalame (Yeremiya 8:7) • Tizilombo (Miyambo 6:6-8; 1 Akorinto 9:26) • Nyama Zapamtunda (Mlaliki 4:6; Afilipi 1:9, 10) 4:20 “Simukudziwa Tsiku Kapena Ola Lake” (Mateyu 24:36; 25:13, 46) 4:55 Nyimbo Na. 27 ndi Pemphero Lomaliza Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZOKHUDZA IFEYO Mudzapezeke nawo Pamsonkhano Wachigawo wa 2024—’Lalikirani Uthenga Wabwino’ Tikukuitanani kuti mudzakhale nawo pamsonkhano wa Mboni za Yehova wachaka chino wa masiku atatu Sindikizani Patsani ena Patsani ena Lachisanu PULOGALAMU YA MSONKHANO WA 2023 LACHISANU | Pulogalamu ya Msonkhano wa 2023—“Khalani Oleza Mtima” Chinenero Chamanja cha ku Malawi LACHISANU | Pulogalamu ya Msonkhano wa 2023—“Khalani Oleza Mtima” https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102023195/univ/art/1102023195_univ_sqr_xl.jpg CO-pgm23 pp. 2-8