Lamlungu YAMBANI Lamlungu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu ‘Yehova akuyembekezera moleza mtima kuti akukomereni mtima’ Yesaya 30:18 M’mawa 9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo 9:30 Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero 9:40 NKHANI YOSIYIRANA: Tengerani Chitsanzo cha Kuleza Mtima kwa Aneneri • Eliya (Yakobo 5:10, 17, 18) • Mika (Mika 7:7) • Hoseya (Hoseya 3:1) • Yesaya (Yesaya 7:3) • Ezekieli (Ezekieli 2:3-5) • Yeremiya (Yeremiya 15:16) • Danieli (Danieli 9:22, 23) 11:05 Nyimbo Na. 142 ndi Zilengezo 11:15 NKHANI YA ONSE: Kodi Mulungu Angakuthandizenidi? (Yesaya 64:4) 11:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda 12:15 Nyimbo Na. 94 ndi Kupuma Masana 1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo 1:45 Nyimbo Na. 114 1:50 VIDIYO: ‘Muzilola Kuti Yehova Akutsogolereni’—Mbali Yachiwiri (Salimo 37:5) 2:30 Nyimbo Na. 115 ndi Zilengezo 2:40 ‘Yehova Akuyembekezera Moleza Mtima Kuti Akukomereni Mtima’ (Yesaya 30:18-21; 60:17; 2 Mafumu 6:15-17; Aefeso 1:9, 10) 3:40 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZOKHUDZA IFEYO Mudzapezeke nawo Pamsonkhano Wachigawo wa 2024—’Lalikirani Uthenga Wabwino’ Tikukuitanani kuti mudzakhale nawo pamsonkhano wa Mboni za Yehova wachaka chino wa masiku atatu Sindikizani Patsani ena Patsani ena Lamlungu PULOGALAMU YA MSONKHANO WA 2023 LAMLUNGU | Pulogalamu ya Msonkhano wa 2023—“Khalani Oleza Mtima” Chinenero Chamanja cha ku Malawi LAMLUNGU | Pulogalamu ya Msonkhano wa 2023—“Khalani Oleza Mtima” https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102023197/univ/art/1102023197_univ_sqr_xl.jpg CO-pgm23 pp. 6-7