Gawo 2 • Machitidwe 6:8–9:43

“Mpingo Umene Unali ku Yerusalemu Unayamba Kuzunzidwa Koopsa”

“Mpingo Umene Unali ku Yerusalemu Unayamba Kuzunzidwa Koopsa”

MACHITIDWE 8:1

Kodi Akhristu a m’nthawi ya atumwi anasiya kuchitira umboni mokwanira za Ufumu wa Mulungu chifukwa choti ankazunzidwa kwambiri? Ayi sanasiye. M’gawoli tiona kuti chizunzo choopsachi chinathandiza Akhristu kuti alalikire kwa anthu ambiri.