PHUNZIRO 1 Mawu Oyamba Abwino YAMBANI Mawu Oyamba Abwino Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Machitidwe 17:22 MFUNDO YAIKULU: M’mawu anu oyamba, muyenera kunena zinthu zochititsa chidwi, kutchula zokhudza nkhani yanu komanso kusonyeza chifukwa chake nkhaniyo ili yothandiza kwambiri kwa omvera. MMENE MUNGACHITIRE: Kukopa chidwi. Sankhani funso, mawu enaake, zochitika zenizeni kapena nkhani imene omvera anu angachite nayo chidwi. Fotokozani nkhani yanu. M’mawu anu oyamba muyenera kuthandiza anthu kudziwa nkhani imene mukambirane komanso cholinga chake. Sonyezani chifukwa chake nkhaniyo ndi yofunika. Konzekerani nkhani yanu m’njira yoti igwirizane ndi zimene zingathandize anthu amene mukukambirana nawo. Anthuwo ayenera kuona mosavuta kuti nkhaniyo iwathandizadi. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mawu Oyamba Abwino KUWERENGA KOMANSO KUPHUNZITSA MWALUSO Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Mawu Oyamba Abwino Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Mawu Oyamba Abwino https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png th phunziro 1