PHUNZIRO 13 Kusonyeza Kuti Nkhaniyo Ndi Yothandiza YAMBANI Kusonyeza Kuti Nkhaniyo Ndi Yothandiza Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Miyambo 3:21 MFUNDO YAIKULU: Thandizani anthu kudziwa mmene mfundo zimene mukuphunzitsa zingawathandizire ndiponso zimene angachite potsatira zimene mukuphunzitsazo. MMENE MUNGACHITIRE: Muziganizira anthu. Muzidzifunsa kuti, Kodi nkhani yangayi ingathandize bwanji anthuwa, nanga mbali zimene zingawathandize kwambiri ndi ziti? Munkhani yanu yonse, muzithandiza anthu kudziwa zoyenera kuchita. Mukangoyamba nkhani yanu, aliyense azizindikira kuti, ‘Nkhaniyitu indithandiza.’ Mukatchula mfundo yaikulu iliyonse, muziwasonyeza mmene angaigwiritsire ntchito. Muzipewa kukamba nkhani mongolambalala popanda kusonyeza zoyenera kuchita. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kusonyeza Kuti Nkhaniyo Ndi Yothandiza KUWERENGA KOMANSO KUPHUNZITSA MWALUSO Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kusonyeza Kuti Nkhaniyo Ndi Yothandiza Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kusonyeza Kuti Nkhaniyo Ndi Yothandiza https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png th phunziro 13