PHUNZIRO 17 Kulankhula Zomveka YAMBANI Kulankhula Zomveka Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu 1 Akorinto 14:9 MFUNDO YAIKULU: Muzilankhula m’njira yoti anthu azimvetsa zimene mukunena. MMENE MUNGACHITIRE: Yesetsani kuti muidziwe bwino nkhani yanu. Mukaidziwa bwino nkhani yanu mukhoza kuifotokoza mosavuta m’mawu anuanu. Muzigwiritsa ntchito ziganizo zifupizifupi zosavuta kumva. Ngakhale kuti pena mukhoza kugwiritsa ntchito ziganizo zitalizitali, muzizidula moyenerera mukamafotokoza mfundo yofunika. Muzifotokoza mawu ovuta. Pewani kugwiritsa ntchito mawu amene anthu sawadziwa. Muzifotokozera mawu ovuta, anthu a m’Baibulo osadziwika kwambiri komanso miyeso ndi zikhalidwe zakale. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kulankhula Zomveka KUWERENGA KOMANSO KUPHUNZITSA MWALUSO Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kulankhula Zomveka Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kulankhula Zomveka https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png th phunziro 17