PHUNZIRO 3 Kugwiritsa Ntchito Mafunso YAMBANI Kugwiritsa Ntchito Mafunso Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Mateyu 16:13-16 MFUNDO YAIKULU: Muzigwiritsa ntchito mafunso oyenera kuti anthu akhale ndi chidwi, kuti mukambirane ndi anthu, komanso kuti mutsindike mfundo zofunika. MMENE MUNGACHITIRE: Muzithandiza anthu kuti akhale ndi chidwi. Muzifunsa mafunso othandiza anthu kuti azifuna kumva zambiri. Muzikambirana ndi anthu. Kuti anthu akhulupirire mfundo zimene mukunena, muyenera kufunsa mafunso angapo owathandiza kuti atsatire mpaka kufika potsimikizira mfundozo. Muzitsindika mfundo zofunika. Funsani funso limene lingachititse anthu kuyembekezera kuti amve mfundo yofunika. Muzifunsa mafunso obwereza pambuyo pa mfundo yofunika iliyonse kapena pomaliza nkhani yanu. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kugwiritsa Ntchito Mafunso KUWERENGA KOMANSO KUPHUNZITSA MWALUSO Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kugwiritsa Ntchito Mafunso Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kugwiritsa Ntchito Mafunso https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png th phunziro 3