PHUNZIRO 4 Kunena Mawu Oyenera Musanayambe Kuwerenga Lemba YAMBANI Kunena Mawu Oyenera Musanayambe Kuwerenga Lemba Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Mateyu 22:41-45 MFUNDO YAIKULU: Muzithandiza anthu kuti akonzekere kumva mfundo inayake pa lemba limene mukufuna kuwerenga. MMENE MUNGACHITIRE: Ganizirani chifukwa chimene mukuwerengera lemba. Pouza anthu lemba limene mukufuna kuliwerenga, muzinena mawu amene angawathandize kuzindikira mfundo yofunika imene angaiphunzire palembalo. Sonyezani kuti Baibulo ndi lothandiza. Ngati mukukambirana ndi anthu amene amakhulupirira zoti kuli Mulungu, muziwathandiza kuona kuti Baibulo ndi “Mawu a Mulungu” ndipo lingatipatse nzeru yapamwamba kwambiri. Muzithandiza anthu kuti akhale ndi chidwi chofuna kumva mfundo yapalembalo. Funsani funso limene yankho lake lili palembalo, tchulani vuto limene njira yolithetsera ikupezeka palembalo kapena tchulani mfundo imene chitsanzo chake chili palembalo. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kunena Mawu Oyenera Musanayambe Kuwerenga Lemba KUWERENGA KOMANSO KUPHUNZITSA MWALUSO Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kunena Mawu Oyenera Musanayambe Kuwerenga Lemba Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kunena Mawu Oyenera Musanayambe Kuwerenga Lemba https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png th phunziro 4