PHUNZIRO 9 Kugwiritsa Ntchito Bwino Zinthu Zooneka YAMBANI Kugwiritsa Ntchito Bwino Zinthu Zooneka Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Genesis 15:5 MFUNDO YAIKULU: Muzigwiritsa ntchito zinthu zooneka kuti anthu amvetse mfundo zikuluzikulu. MMENE MUNGACHITIRE: Muzisankha zinthu zimene zingathandizedi pophunzitsa. Mungagwiritse ntchito zithunzi, mapu, matchati kapena zinthu zina pofuna kutsindika mfundo zofunika osati timfundo ting’onoting’ono. Mukamaliza, anthu azikumbukira mfundo yaikuluyo osati zinthu zooneka zokhazo. Zinthuzo zizikhala zoti aliyense atha kuziona. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kugwiritsa Ntchito Bwino Zinthu Zooneka KUWERENGA KOMANSO KUPHUNZITSA MWALUSO Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kugwiritsa Ntchito Bwino Zinthu Zooneka Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kugwiritsa Ntchito Bwino Zinthu Zooneka https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png th phunziro 9