Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani


Mavidiyo ndi Zinthu Zina za Gawo 3

Mavidiyo ndi Zinthu Zina za Gawo 3

 34 Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Yehova?

ONANI ZINANSO

 35 N’chiyani Chingatithandize Kuti Tizisankha Zinthu Mwanzeru?

ONANI ZINANSO

“Kodi Mumafunikira Lamulo la M’Baibulo Nthawi Zonse?” (Nsanja ya Olonda, December 1, 2003)

 36 Muzichita Zinthu Zonse Moona Mtima

ONANI ZINANSO

“Kodi Muyenera Kukhoma Misonkho?” (Nsanja ya Olonda, September 1, 2011)

 37 Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Ntchito Komanso Ndalama

ONANI ZINANSO

 38 Muziona Kuti Moyo Ndi Mphatso Yamtengo Wapatali

ONANI ZINANSO

“‘Masewera Angozi’​—Kodi Muyenera Kuika Moyo Wanu Pachiswe Mwakuwachita?” (Galamukani!, October 8, 2000)

 39 Mmene Mulungu Amaonera Magazi

ONANI ZINANSO

“Ndinayamba Kuona Magazi Mmene Mulungu Amawaonera” (Galamukani!, December 8, 2003)

 40 Tingatani Kuti Mulungu Azitiona Kuti Ndife Oyera?

“Kodi Ndingatani Kuti Ndisiye Chizolowezi Choseweretsa Maliseche?” (Mayankho a Zimene Achinyamata Amadzifunsa, Buku Loyamba, mutu 25)

ONANI ZINANSO

“N’zotheka Kusiya Fodya” (Galamukani!, May 2010)

 41 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Kugonana?

Thawani Dama (5:06)

ONANI ZINANSO

“Kodi Kugonana Kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha N’kolakwika?” (Nkhani yapawebusaiti)

“Kodi Kugonana M’kamwa Kumakhaladi Kugonana?” (Nkhani yapawebusaiti)

“Baibulo Limasintha Anthu” (Nsanja ya Olonda, April 1, 2011)

 42 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yokhala Pabanja Ndi Kusakhala Pabanja?

ONANI ZINANSO

“Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga” (Nsanja ya Olonda, July 1, 2004)

 43 Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani ya Mowa?

ONANI ZINANSO

“Khalani ndi Maganizo Oyenera Pankhani ya Kumwa Mowa” (Nsanja ya Olonda, January 1, 2010)

“Mafunso Ochokera kwa Owerenga” (Nsanja ya Olonda, February 15, 2007)

“Baibulo Limasintha Anthu” (Nsanja ya Olonda, May 1, 2012)

 44 Kodi Zikondwerero Zonse Zimasangalatsa Mulungu?

ONANI ZINANSO

“N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sachita Nawo Maholide Ena?” (Nkhani yapawebusaiti)

“N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sakondwerera Masiku Akubadwa?” (Nkhani yapawebusaiti)

“Amasangalala Ngakhale Kuti Sachita Khirisimasi” (Nsanja ya Olonda, December 1, 2012)

 45 Kodi Kusakhala Mbali ya Dziko Kumatanthauza Chiyani?

ONANI ZINANSO

“Yense Adzasenza Katundu Wake wa Iye Mwini” (Nsanja ya Olonda, March 15, 2006)

 46 N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudzipereka Ndiponso Kubatizidwa?

ONANI ZINANSO

“N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudzipereka kwa Yehova?” (Nsanja ya Olonda, January 15, 2010)

“Baibulo Limasintha Anthu” (Nsanja ya Olonda, November 1, 2012)

 47 Kodi Mwakonzeka Kubatizidwa?

ONANI ZINANSO