Kodi Mwasangalala Ndi Zimene Mwaphunzira? YAMBANI Kodi Mwasangalala Ndi Zimene Mwaphunzira? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi Kodi mungakonde kudziwa zambiri zimene Baibulo limaphunzitsa? Iyi ndi mbali yochepa chabe ya zimene mungaphunzire m’buku la Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana. Palibe amene adzakuuzeni kuti mugule bukuli kapenanso kuti mulipire kuti muziphunzira. Tidzasangalala kuphunzira nanu pa nthawi ndi malo amene mungasankhe. Mukamaphunzira Baibulo pogwiritsa ntchito bukuli muphunzira nkhani zambiri kuphatikizapo: Cholinga cha moyo Zimene mungachite kuti mupeze mtendere weniweni Zimene mabanja angachite kuti azisangalala Zimene Baibulo limalonjeza zokhudza m’tsogolo Kuti mupeze bukuli komanso kuti mupitirize kuphunzira Baibulo, pemphani wa Mboni za Yehova aliyense kapenanso lembani fomu yopempha phunziro la Baibulo kudzera pa jw.org. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kodi Mwasangalala Ndi Zimene Mwaphunzira? Kodi Mwasangalala Ndi Zimene Mwaphunzira? Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kodi Mwasangalala Ndi Zimene Mwaphunzira? https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102021807/univ/art/1102021807_univ_sqr_xl.jpg lffi