ZAKUMAPETO B Kusiya Kukambirana ndi Munthu YAMBANI Kusiya Kukambirana ndi Munthu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Ngati munthu sakuvomereza mfundo inayake kapena akufunsa kuti adziwe bwino zina zake, timakhala okonzeka kumuthandiza. Timafuna tizikambirana ndi anthu omwe ali ndi ‘maganizo abwino amene angawathandize kukapeza moyo wosatha.”—Mac. 13:48. Koma bwanji ngati ndi waukali, akungofuna zokangana kapenanso sakufuna kuti ticheze naye? Tingasiye kukambirana naye, modekha komanso mwaulemu. (Miy. 17:14) Ngati titasiyana naye bwino, zingakhale zosavuta kudzachezanso naye m’tsogolo.—1 Pet. 2:12. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kusiya Kukambirana ndi Munthu MUZIKONDA ANTHU—MUZIWAPHUNZITSA Kusiya Kukambirana ndi Munthu Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kusiya Kukambirana ndi Munthu https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/442e614bdf/images/syn_placeholder_sqr.png lmd