CHIGAWO 11 Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu? YAMBANI Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Mulungu amamva mapemphero athu. 1 Petulo 3:12 Yehova ndi “Wakumva pemphero.” (Salimo 65:2) Iye amafuna kuti tizimuuza zakukhosi kwathu. Muzipemphera kwa Yehova yekha osati kwa wina aliyense. Pali zinthu zambiri zimene tingatchule popemphera. 1 Yohane 5:14 Muzipemphera kuti chifuniro cha Mulungu chichitike kumwamba komanso padziko lapansi pano. Muzipemphera m’dzina la Yesu, kuti musonyeze kuti mumayamikira zimene iye anakuchitirani. Pemphani Yehova kuti akuthandizeni kuchita zinthu zabwino. Mungapemphe zinthu monga chakudya, ntchito, nyumba, zovala ndiponso thanzi labwino. Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ESSENTIAL BIBLE TEACHINGS Kodi Mulungu Amamvetsera Mapemphero Onse? Nanga bwanji ngati munthu akupempha zinthu zinazake chifukwa cha dyera? Bwanji ngati mwamuna atamenya mkazi wake, kenako n’kumapempha Mulungu kuti amudalitse? Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu? MVERANI MULUNGU KUTI MUDZAPEZE MOYO WOSATHA Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu? Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu? https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/f62df3bf2a/images/syn_placeholder_sqr.png