CHIGAWO 14 Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Ndinu Wokhulupirika kwa Yehova? YAMBANI Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Ndinu Wokhulupirika kwa Yehova? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Khalani kumbali ya Mulungu. 1 Petulo 5:6-9 Muzipewa kuchita nawo miyambo yosagwirizana ndi Baibulo. Munthu amafunika kulimba mtima kuti achite zimenezi. Musamachite nawo ndale zadzikoli chifukwa sizigwirizana ndi zofuna za Yehova ndi Ufumu wake. Sankhani mwanzeru, mverani Mulungu. Mateyu 7:24, 25 Muzipita kumisonkhano ya Mboni za Yehova ndipo iwo adzakuthandizani kuti muyandikire Mulungu. Pitirizani kuphunzira za Mulungu ndipo muziyesetsa kumvera malamulo ake. Chikhulupiriro chanu chikalimba, muyenera kupereka moyo wanu kwa Yehova ndi kubatizidwa.—Mateyu 28:19. Muzimvera Mulungu. Muziwerenga Baibulo, ndipo pemphani aliyense wa Mboni za Yehova kuti akuthandizeni kulimvetsa. Kenako, muzigwiritsa ntchito zimene mwaphunzirazo. Mukamachita zimenezi mudzapeza moyo wosatha.—Salimo 37:29. Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi MISONKHANO Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? Onani mkati mwa Nyumba ya Ufumu kuti mudziwe zimene zimachitika. ZOKHUDZA IFEYO Pemphani Kuti Tidzakuyendereni Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova. ZOKHUDZA IFEYO Fikani Pamsonkhano Dziwani zambiri zokhudza misonkhano yathu. Pezani malo apafupi amene kumachitikira misonkhano yathu. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Ndinu Wokhulupirika kwa Yehova? MVERANI MULUNGU KUTI MUDZAPEZE MOYO WOSATHA Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Ndinu Wokhulupirika kwa Yehova? Chinenero Chamanja cha ku Malawi Kodi Mungasonyeze Bwanji Kuti Ndinu Wokhulupirika kwa Yehova? https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/e781f8601f/images/syn_placeholder_sqr.png