Lachisanu YAMBANI Lachisanu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu “Uthenga wabwino wa chimwemwe chachikulu chimene anthu onse adzakhale nacho”—Luka 2:10 M’mawa 8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo 8:30 Nyimbo Na. 150 Komanso Pemphero 8:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: N’chifukwa Chiyani Tikufunikira Uthenga Wabwino? (1 Akorinto 9:16; 1 Timoteyo 1:12) 9:10 VIDIYO: Uthenga Wabwino wa Yesu: Gawo 1 Kuwala Kwenikweni kwa Dziko—Mbali Yoyamba (Mateyu 1:18-25; Luka 1:1-80; Yohane 1:1-5) 9:45 Nyimbo Na. 96 Komanso Zilengezo 9:55 NKHANI YOSIYIRANA: ‘Anatsogoleredwa ndi Mzimu Woyera’ • Mateyu (2 Petulo 1:21) • Maliko (Maliko 10:21) • Luka (Luka 1:1-4) • Yohane (Yohane 20:31) 11:10 Nyimbo Na. 110 Komanso Kupuma Masana 12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo 12:45 Nyimbo Na. 117 12:50 NKHANI YOSIYIRANA: Muzikhulupirira Choonadi Chokhudza Yesu • Mawu (Yohane 1:1; Afilipi 2:8-11) • Dzina Lake (Machitidwe 4:12) • Kubadwa Kwake (Mateyu 2:1, 2, 7-12, 16) 1:30 Nyimbo Na. 99 Komanso Zilengezo 1:40 NKHANI YOSIYIRANA: Zomwe Tikuphunzira pa Moyo wa M’nthawi ya Yesu • Malo (Deuteronomo 8:7) • Nyama (Luka 2:8, 24) • Chakudya (Luka 11:3; 1 Akorinto 10:31) • Moyo Wapakhomo (Afilipi 1:10) • Moyo Wapamudzi (Deuteronomo 22:4) • Maphunziro (Deuteronomo 6:6, 7) • Kulambira (Deuteronomo 16:15, 16) 3:15 N’chifukwa Chiyani Uthenga Wabwino Umatchulidwa Kuti ndi ‘Uthenga Wosatha’? (Chivumbulutso 14:6, 7) 3:50 Nyimbo Na. 66 Komanso Pemphero Lomaliza Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZOKHUDZA IFEYO Mudzapezeke nawo Pamsonkhano Wachigawo wa 2024—’Lalikirani Uthenga Wabwino’ Tikukuitanani kuti mudzakhale nawo pamsonkhano wa Mboni za Yehova wachaka chino wa masiku atatu MISONKHANO IKULUIKULU Mukuitanidwa ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2024 Wakuti ‘Lalikirani Uthenga Wabwino’ Tikukuitanani kuti mudzakhale nafe pamsonkhano wa Mboni za Yehova wa masiku atatu wachaka chino. MISONKHANO IKULUIKULU Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Onerani zimene zili muvidiyo yoyamba yakuti Moyo wa Yesu Komanso Utumiki Wake. Vidiyo imeneyi idzaonetsedwa pamsonkhano wa 2024. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Lachisanu PULOGALAMU YA MSONKHANO WA 2024 LACHISANU | Pulogalamu ya Msonkhano wa 2024—‘Lalikirani Uthenga Wabwino’ Chinenero Chamanja cha ku Malawi LACHISANU | Pulogalamu ya Msonkhano wa 2024—‘Lalikirani Uthenga Wabwino’ https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102024194/univ/art/1102024194_univ_sqr_xl.jpg CO-pgm24