Lamlungu YAMBANI Lamlungu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu “. . . kenako mapeto adzafika”—Mateyu 24:14 M’mawa 8:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo 8:30 Nyimbo Na. 84 Komanso Pemphero 8:40 NKHANI YOSIYIRANA: Muzitsanzira Anthu Amene Ankakhulupirira Uthenga Wabwino • Zekariya (Aheberi 12:5, 6) • Elizabeti (1 Atesalonika 5:11) • Mariya (Salimo 77:12) • Yosefe (Miyambo 1:5) • Simiyoni ndi Ana (1 Mbiri 16:34) • Yesu (Yohane 8:31, 32) 10:05 Nyimbo Na. 65 Komanso Zilengezo 10:15 NKHANI YA ONSE: N’chifukwa Chiyani Sitimaopa Uthenga Woipa? (Salimo 112:1-10) 10:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda 11:15 Nyimbo Na. 61 Komanso Kupuma Masana 12:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo 12:45 Nyimbo Na. 122 12:50 KUWERENGA BAIBULO MWASEWERO: “Nthawi Yodikira Yatha” (Chivumbulutso 10:6) 1:20 Nyimbo Na. 126 Komanso Zilengezo 1:30 Kodi Mwaphunzira Chiyani? 1:40 N’chifukwa Chiyani Tikufunika ‘Kugwira Mwamphamvu Uthenga Wabwino’ Nanga Tingachite Bwanji Zimenezi? (1 Akorinto 2:16; 15:1, 2, 58; Maliko 6:30-34) 2:30 Nyimbo Yatsopano Komanso Pemphero Lomaliza Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZOKHUDZA IFEYO Mudzapezeke nawo Pamsonkhano Wachigawo wa 2024—’Lalikirani Uthenga Wabwino’ Tikukuitanani kuti mudzakhale nawo pamsonkhano wa Mboni za Yehova wachaka chino wa masiku atatu MISONKHANO IKULUIKULU Mukuitanidwa ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2024 Wakuti ‘Lalikirani Uthenga Wabwino’ Tikukuitanani kuti mudzakhale nafe pamsonkhano wa Mboni za Yehova wa masiku atatu wachaka chino. MISONKHANO IKULUIKULU Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Onerani zimene zili muvidiyo yoyamba yakuti Moyo wa Yesu Komanso Utumiki Wake. Vidiyo imeneyi idzaonetsedwa pamsonkhano wa 2024. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Lamlungu PULOGALAMU YA MSONKHANO WA 2024 LAMLUNGU | Pulogalamu ya Msonkhano wa 2024—‘Lalikirani Uthenga Wabwino’ Chinenero Chamanja cha ku Malawi LAMLUNGU | Pulogalamu ya Msonkhano wa 2024—‘Lalikirani Uthenga Wabwino’ https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102024196/univ/art/1102024196_univ_sqr_xl.jpg CO-pgm24