Nthawi Imene Zinthu Zosiyanasiyana Zinachitika YAMBANI Nthawi Imene Zinthu Zosiyanasiyana Zinachitika Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu “Pa chiyambi . . .” 4026 B.C.E. Adamu analengedwa 3096 B.C.E. Adamu anafa 2370 B.C.E. Chigumula chinayamba 2018 B.C.E. Abulahamu anabadwa 1943 B.C.E. Pangano la Abulahamu 1750 B.C.E. Yosefe anagulitsidwa ku ukapolo chaka cha 1613 B.C.E. chisanafike Mayesero a Yobu 1513 B.C.E. Ulendo wochoka ku Iguputo 1473 B.C.E. Aisiraeli analowa m’dziko la Kanani motsogoleredwa ndi Yoswa 1467 B.C.E. Anagonjetsa mbali yaikulu ya dziko la Kanani 1117 B.C.E. Sauli anadzozedwa kukhala mfumu 1070 B.C.E. Mulungu analonjeza Davide kuti adzam’patsa ufumu 1037 B.C.E. Solomo anakhala mfumu 1027 B.C.E. Anamaliza kumanga kachisi ku Yerusalemu cha m’ma 1020 B.C.E. Anamaliza kulemba Nyimbo ya Solomo 997 B.C.E. Ufumu wa Isiraeli unagawanika cha m’ma 717 B.C.E. Ntchito yolemba buku la Miyambo inatha mu 607 B.C.E. Yerusalemu anawonongedwa; Aisiraeli anapita ku ukapolo ku Babulo 539 B.C.E. Babulo anagonjetsedwa ndi Koresi 537 B.C.E. Ayuda amene anali ku ukapolo anabwerera ku Yerusalemu 455 B.C.E. Anamanganso mpanda wa Yerusalemu; kuyambika kwa masabata 69 a zaka 443 B.C.E. itadutsa Malaki anamaliza kulemba buku lake la ulosi Yesu anabadwa cha m’ma 2 B.C.E. 29 C.E. Yesu anabatizidwa ndipo anayamba kulalikira za Ufumu wa Mulungu 31 C.E. Yesu anasankha atumwi 12; analalikira paphiri 32 C.E. Yesu anaukitsa Lazaro Nisan 14, 33 C.E. Yesu anapachikidwa (Mwezi wa Nisani umayamba mkatikati mwa March ndipo umathera mkatikati mwa April) Nisan 16, 33 C.E. Yesu anaukitsidwa Sivani 6, 33 C.E. Pentekosite; kulandira mzimu woyera (Mwezi wa Sivani umayamba mkatikati mwa May ndipo umathera mkatikati mwa June) 36 C.E. Koneliyo akhala Mkhristu cha m’ma 47-48 C.E. Ulendo woyamba wa Paulo wopita kukalalikira cha m’ma 49-52 C.E. Ulendo wachiwiri wa Paulo wopita kukalalikira cha m’ma 52-56 C.E. Ulendo wachitatu wa Paulo wopita kukalalikira 60-61 C.E. Paulo analemba makalata ali m’ndende ku Roma chaka cha 62 C.E. chisanafike Yakobo, m’bale wake wa Yesu, analemba kalata 66 C.E. Ayuda anagalukira Aroma 70 C.E. Aroma anawononga Yerusalemu ndi kachisi cha m’ma 96 C.E. Yohane analemba buku la Chivumbulutso cha m’ma 100 C.E. Yohane, mtumwi womalizira anamwalira Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Nthawi Imene Zinthu Zosiyanasiyana Zinachitika KODI BAIBULO LILI NDI UTHENGA WOTANI? Nthawi Imene Zinthu Zosiyanasiyana Zinachitika Chinenero Chamanja cha ku Malawi Nthawi Imene Zinthu Zosiyanasiyana Zinachitika https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png bm