Kodi mukufuna kudziwa zambiri? YAMBANI Kodi mukufuna kudziwa zambiri? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Munthu wina wanzeru analemba kuti: “Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri. Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.” (Miyambo 4:7) Mlengi wathu amatithandiza kuti tikhale ndi nzeru komanso kuti tizimvetsa bwino zinthu n’cholinga choti tizisankha zinthu mwanzeru n’kumakhala ndi moyo wosangalala. Ngati mukufuna kudziwa zambiri zokhudza nzeru zothandiza zomwe zimapezeka m’Baibulo, pitani pa jw.org. Pamenepa mupezapo zinthu monga . . . BAIBULO MAVIDIYO MAKATUNI ZOCHITIKA PA MOYO WA ANTHU ENA NKHANI Zonsezi zikupezeka mwaulere ndipo ndi zothandiza kwa anthu a misinkhu yonse komanso ochokera kulikonse. Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ESSENTIAL BIBLE TEACHINGS N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika? Anthu ambiri amafuna kudziwa kuti n’chifukwa chiyani padzikoli pali mavuto ambiri. Baibulo limapereka yankho logwira mtima pa nkhaniyi. ESSENTIAL BIBLE TEACHINGS Kodi Mulungu Ali Ndi Dzina? Mulungu ali ndi maina ambiri audindo monga akuti Atate, Mlengi ndi Ambuye. Koma Dzina lake lenileni limapezeka m’Baibulo malo oposa 7000. ZOKHUDZA IFEYO Pemphani Kuti Tidzakuyendereni Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kodi mukufuna kudziwa zambiri? GALAMUKANI! Nzeru—Kodi mukufuna kudziwa zambiri? Chinenero Chamanja cha ku Malawi Nzeru—Kodi mukufuna kudziwa zambiri? https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/102021012/univ/art/102021012_univ_sqr_xl.jpg g21.1 11