Nzeru Zothandiza Kukhala Ndi Moyo Wosangalala YAMBANI Nzeru Zothandiza Kukhala Ndi Moyo Wosangalala Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu “Ngakhale kuti nthawi zina ndimakhumudwa ndi zinthu zoipa zimene zikuchitika m’dzikoli monga nkhondo, umphawi, matenda komanso kuchitiridwa nkhanza kwa ana, ndili ndi chiyembekezo kuti zimenezi zidzatha.”—RANI. * Rani anapeza chimwemwe chenicheni ataphunzira kuti Mlengi wathu, yemwe ndi Mulungu wamphamvuyonse, ndi amene amapereka nzeru zothandiza. Mukamawerenga mfundo zotsatirazi, onani mmene mfundo zomwe Mulungu akutiphunzitsa zingakuthandizireni kuti . . . mukhale ndi banja losangalala muzikhala mwamtendere ndi anthu ena muzikhala okhutira mudziwe chomwe chimachititsa kuti tizivutika komanso kufa mukhale ndi chiyembekezo chabwino cha m’tsogolo mumudziwe bwino Mlengi wathu komanso mukhale mnzake Muonanso kuti Mlengi wathu samangopereka nzeru kwa anthu ochepa, koma amazipereka kwa wina aliyense amene amazifunafuna. ^ ndime 2 Mayina asinthidwa m’magaziniyi. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Nzeru Zothandiza Kukhala Ndi Moyo Wosangalala GALAMUKANI! Nzeru Zothandiza Kukhala Ndi Moyo Wosangalala Chinenero Chamanja cha ku Malawi Nzeru Zothandiza Kukhala Ndi Moyo Wosangalala https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/102021004/univ/art/102021004_univ_sqr_xl.jpg g21.1 3