Mfundo Zina Zothandiza Mabanja

Mfundo Zina Zothandiza Mabanja

BAIBULO LIMAPEREKA MALANGIZO OTHANDIZA KWAMBIRI kwa anthu okwatirana, makolo komanso kwa achinyamata. Malangizo ake angakuthandizeni kukhala oganiza bwino komanso kusankha bwino zochita.​—Miyambo 1:1-4.

BAIBULO LIMAYANKHANSO MAFUNSO OFUNIKA KWAMBIRI MONGA:

Tikukulimbikitsani kuti mufufuze m’Baibulo mayankho a mafunso amenewa komanso ena. Onerani kavidiyo kakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? popanga sikani kachidindo aka kapena pitani pa www.pr418.com/ny.