Dziwani Zambiri pa JW.ORG

Dziwani Zambiri pa JW.ORG

Kodi ndi nkhani iti imene mukufuna kuidziwa bwino?

Mmene ndingalimbitsire banja langa

Onani nkhani yakuti “Kodi Mungatani Kuti Zipangizo Zamakono Zisamakusokonezeni?

Mmene ndingaphunzitsire ana anga makhalidwe abwino

Onani nkhani yakuti “Phunzitsani Ana Anu Kugwiritsa Ntchito Foni Mosamala.”

Mmene ndingachepetsere kuda nkhawa ndi zinthu zam’tsogolo

Onani nkhani ya pachikuto ya mutu wakuti “Kodi M’tsogolomu Muli Zotani?

Baibulo lingakuthandizeni inuyo komanso banja lanu kuti muzikhala ndi moyo wabwino panopa komanso kuti mukhale ndi chiyembekezo chodalirika cha zinthu zam’tsogolo.