Zimene Zili M’magaziniyi

Zimene Zili M’magaziniyi

Zipangizo zamakono zikhoza kusokoneza anthu pang’ono ndi pang’ono komanso m’njira yoti sangathe kuizindikira.

KODI ZIPANGIZO ZAMAKONO ZIMAKHUDZA BWANJI . . .

  • Ubwenzi Wanu ndi Anzanu?

  • Ana Anu?

  • Banja Lanu?

  • Mmene Mumaganizira?