ZOTI NDIPHUNZIRE Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru YAMBANI Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Werengani Genesis 25:29-34 kuti muone ngati Esau ndi Yakobo anasankha zinthu mwanzeru. Fufuzani mozama nkhani yake. Kodi n’chiyani chinachitika poyamba? (Gen. 25:20-28) Nanga n’chiyani chinachitika pambuyo pake?—Gen. 27:1-46. Fufuzani mozama mfundo zake. Kodi pa nthawiyo mwana woyamba ankakhala ndi ufulu komanso udindo uti?—Gen. 18:18, 19; lfb 12:3. Kodi nthawi zonse kukhala mwana woyamba kunkaphatikizapo kukhala kholo la Mesiya? (w17.12 14-15) Onani zimene mukuphunzirapo, ndipo muzizitsatira. Mosiyana ndi Esau, n’chifukwa chiyani Yakobo ankaona kuti kukhala mwana woyamba n’kofunika kwambiri? (Aheb. 12:16, 17; lfb 12) Kodi Yehova ankawaona bwanji anthu awiriwa, nanga n’chifukwa chiyani? (Mal. 1:2, 3) Kodi Esau ankafunika kuchita chiyani kuti asankhe zinthu mwanzeru? Dzifunseni kuti: ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimayamikira zinthu zauzimu mlungu uliwonse, mwachitsanzo poonetsetsa kuti tikuchita kulambira kwa pabanja?’ Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru Chinenero Chamanja cha ku Malawi Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/1add6d1d93/images/syn_placeholder_sqr.png w24.4 103