Kodi Tingathetse Bwanji Chidani?

Kodi Tingathetse Bwanji Chidani?

Baibulo, lomwe ndi Mawu a Mulungu lili ndi mphamvu zothandiza munthu kusintha makhalidwe ake. (Aheberi 4:12) Zimene limaphunzitsa zathandiza anthu ambiri kusiya kudana ndi anthu ena. Tiyeni tione mfundo 4 zimene Baibulo limaphunzitsa zomwe zathandiza anthu ambiri kuthetsa chidani.