Mulungu Akulonjeza Kuti Kuvutika Maganizo Kudzatheratu YAMBANI Mulungu Akulonjeza Kuti Kuvutika Maganizo Kudzatheratu Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kudzera m’Baibulo, Mulungu amapereka malangizo komanso amatonthoza anthu amene akuvutika ndi matenda amaganizo. Kuwonjezera pamenepo, iye akulonjeza kuti adzathetseratu zinthu zimene zimachititsa kuti anthu azivutika ndi matenda amaganizo. Mulungu akadzakwaniritsa lonjezo limeneli, sitidzamvanso kuwawa kulikonse, kuvutika ndi nkhawa kapena maganizo oipa chifukwa “zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso ndipo sizidzabweranso mumtima.”—Yesaya 65:17. A Mboni za Yehova adzasangalala kukuthandizani kudziwa nthawi imene Mulungu adzakwaniritse lonjezo lokhazika mtima pansi limeneli komanso mmene adzachitire zimenezi. Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi Mfundo Zofunika za M'Baibulo—Mavidiyo Kodi N’zotheka Kukhala pa Ubwenzi ndi Mulungu? Kwa zaka zambiri anthu akhala akufuna kudziwa amene anawalenga. Baibulo lingatithandize kuti tikhale mnzake wa Mulungu. Ubwenzi umenewu umayamba tikadziwa dzina la Mulungu. ZOKHUDZA IFEYO Pemphani Kuti Tidzakuyendereni Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mulungu Akulonjeza Kuti Kuvutika Maganizo Kudzatheratu NSANJA YA OLONDA Mulungu Akulonjeza Kuti Kuvutika Maganizo Kudzatheratu Chinenero Chamanja cha ku Malawi Mulungu Akulonjeza Kuti Kuvutika Maganizo Kudzatheratu https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/2023010/univ/art/2023010_univ_sqr_xl.jpg wp23 No. 1 p. 9