Mungaphunzirenso Izi YAMBANI Mungaphunzirenso Izi Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kodi mumakonda kuwerenga mbiri ya moyo wa abale ndi alongo athu? Banja lina lomwe limawerenga nkhani imodzi m’mawa uliwonse linati: “Nkhanizi zimatilimbikitsa komanso kutithandiza kukhala osangalala. Zimatikumbutsa kuti nafenso tingakhale okhulupirika pa chilichonse.” Mlongo winanso yemwe amamva choncho analemba kuti: “Nkhanizi ndi zotonthoza, zolimbikitsa komanso zokhazika mtima pansi. Mbiri ya abale ndi alongo omwe amafotokozedwa imasonyeza kuti moyo wawo ndi watanthauzo. Zimandilimbikitsa kuti ndizichita zambiri mu utumiki komanso kuthandiza ana anga kuti adzachite utumiki wa nthawi zonse.” Nkhanizi zingakuthandizeni kuti muzichita zambiri potumikira Yehova, musiye makhalidwe oipa komanso muzipirira mosangalala ndiponso mokhulupirika mayesero ovuta. Kodi mungapeze bwanji nkhanizi? Fufuzani pa gawo lakuti “Mbiri za a Mboni za Yehova Ena” pa jw.org kapena pa JW Library®. Fufuzani “Mbiri za a Mboni za Yehova Ena” pa Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI kapena Watchtower Library. Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Mungaphunzirenso Izi NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA Mungaphunzirenso Izi Chinenero Chamanja cha ku Malawi Mungaphunzirenso Izi https://assetsnffrgf-a.akamaihd.net/assets/ct/f62df3bf2a/images/syn_placeholder_sqr.png w23 January