NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA October 2023

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira December 11, 2023–January 7, 2024.

1923​—⁠Zimene Zinachitika Zaka 100 Zapitazo

M’chaka cha 1923, Ophunzira Baibulo anasintha mmene ankachitira misonkhano komanso mmene ankagwirira ntchito yolalikira zomwe zinachititsa kuti ayambe kugwirizana kwambiri, ndipo mgwirizano umenewo ndi umene ulipo mpaka lero.

NKHANI YOPHUNZIRA 42

Kodi Ndinu ‘Okonzeka Kumvera’?

Studied Idzaphunziridwa mlungu wa December 11-17, 2023.

NKHANI YOPHUNZIRA 43

Yehova “Adzakulimbitsani”

Idzaphunziridwa mlungu woyambira December 18-24, 2023.

NKHANI YOPHUNZIRA 44

Muzichita Khama Kuti Muzimvetsa Bwino Mawu a Mulungu

Idzaphunziridwa mlungu woyambira December 25-31, 2023.

NKHANI YOPHUNZIRA 45

Muziyamikira Mwayi Wanu Wolambira M’kachisi Wauzimu wa Yehova

Idzaphunziridwa mlungu woyambira January 1-7, 2024.