NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA September 2024
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira November 11–December 8, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 36
“Muzichita Zimene Mawu Amanena”
Idzaphunziridwa mlungu woyambira November 11-17, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 37
Kalata Imene Ingatithandize Kupirira Mokhulupirika Mpaka Mapeto
Idzaphunziridwa mlungu woyambira November 18-24, 2024.
MBIRI YA MOYO WANGA
Moyo Wabwino Kwambiri Potumikira Yehova
André Ramseyer wakhala mu utumiki wa nthawi zonse kwa zaka 70 ndipo wakhala akugwira ntchito zosiyanasiyana. Kodi ndi mavuto ati amene anakumana nawo, nanga wasonyeza bwanji kuti amaika Yehova pamalo oyamba?
Mafunso Ochokera kwa Owerenga
Kodi ophunzira 70 omwe Yesu anawatuma kukalalikira aja, anali kuti pomwe iye ankayambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye? Kodi anali atamusiya?
NKHANI YOPHUNZIRA 38
Kodi Mumamvera Machenjezo?
Idzaphunziridwa mlungu wa November 25–December 1, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 39
Kupatsa Kumatichititsa Kukhala Osangalala
Idzaphunziridwa mlungu woyambira December 2-8, 2024.
Muzikhala Okonzeka Kuphunzira Zinthu Zatsopano
Kodi tingatani kuti pophunzira patokha tizimvetsa zimene Yehova akutiphunzitsa?