NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA August 2018

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa October 1-28, 2018.

Kodi Mukudziwa Nkhani Yonse?

Kodi ndi mfundo zitatu ziti za m’Baibulo zimene zingatithandize kuganizira bwino nkhani iliyonse n’kuzindikira zoona zake?

Tisamaweruze Poona Maonekedwe Akunja

Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zitatu zimene tiyenera kupewa pa nkhani yoweruza anthu.

Anthu Opatsa Amakhala Osangalala

Kodi kukhala opatsa kumathandiza bwanji kuti munthu akhale wosangalala?

Tizigwira Ntchito ndi Yehova Tsiku Lililonse

Kodi tingagwire ntchito ndi Yehova m’njira 5 ziti?