NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA May 2024
M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira July 8–August 11, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 18
Muzikhulupirira “Woweruza wa Dziko Lonse Lapansi” Yemwe Ndi Wachifundo
Idzaphunziridwa mlungu woyambira July 8-14, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 19
Kodi Tikudziwa Chiyani pa Nkhani ya Mmene Yehova Adzaweruzire Anthu?
Idzaphunziridwa mlungu woyambira July 15-21, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 20
Chikondi Chizikulimbikitsani Kuti Mupitirize Kulalikira
Idzaphunziridwa mlungu woyambira July 22-28, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 21
Kodi Mungatani Kuti Mupeze Munthu Wokwatirana Naye?
Idzaphunziridwa mlungu woyambira July 29–August 4, 2024.
NKHANI YOPHUNZIRA 22
Kodi Mungatani Kuti Chibwenzi Chanu Chiziyenda Bwino?
Idzaphunziridwa mlungu woyambira August 5-11, 2024.