NSANJA YA OLONDA October 2014

NKHANI YAPACHIKUTO

Yesu Ankaona Kuti Ufumu wa Mulungu Ndi Wofunika Kwambiri

Yesu ankakonda kuuza anthu zokhudza Ufumu wa Mulungu kuposa nkhani iliyonse chifukwa ankadziwa kuti Ufumuwu ndi wofunika kwambiri.

A CONVERSATION WITH A NEIGHBOR

Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulira? (Gawo 1)

Ngati mukudziwa yankho lake, kodi mungamufotokozere munthu wina bwinobwino kuchokera m’Baibulo?

THE BIBLE CHANGES LIVES

Ndinali Munthu Wodzikonda Kwambiri

Christof Bauer ankawerenga Baibulo ali m’boti pakati pa nyanja ya Atlantic. Kodi anaphunzira zotani?