Nkhani ya Yona—Yophunzitsa Kulimba Mtima Komanso Chifundo

KOPERANI

Watchtower LAIBULALE YA PA INTANET™

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

Yona—Anaphunzira pa Zolakwa Zake

Kodi mungamvetse chifukwa chake Yona ankaopa kugwira ntchito imene Mulungu anamupatsa? Nkhani ya Yona ikutiphunzitse zambiri zokhudza kuleza mtima ndiponso chifundo cha Yehova.

TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO

Yona—Anaphunzira Kufunika Kochitira Ena Chifundo

Kodi nkhani ya Yona ingatithandize bwanji kudzifufuza?