Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Aefeso

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Aefeso

Onerani vidiyoyi kuti muone mfundo zachidule za m’kalata yopita kwa Aefeso. Kalatayi ikusonyeza kuti Mulungu ali ndi cholinga choti adzabweretse mtendere komanso mgwirizano kudzera mwa Yesu Khristu.