Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Chivumbulutso

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Chivumbulutso

Onerani vidiyoyi kuti muone mmene masomphenya a m’buku la Chivumbulutso amasonyezera zimene Ufumu wa Mulungu udzachite pofuna kukwaniritsa cholinga chimene Mulungu anali nacho kwa anthu ndi dziko lapansili.