Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Zekariya

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Zekariya

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zachidule za m’buku la Zekariya. Bukuli limafotokoza zambiri zokhudza kubwera kwa Mesiya, kuperekedwa kwake komanso imfa yake.