Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yuda

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yuda

Yuda anagwiritsa ntchito mafanizo ochititsa chidwi pofuna kuthandiza Akhristu kuzindikira anthu omwe ankafuna kulowetsa ziphunzitso zabodza komanso makhalidwe oipa mumpingo.