Esitere Anali Wolimba Mtima YAMBANI Esitere Anali Wolimba Mtima Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Pangani Dawunilodi: Manotsi 1. Anali wamasiye Komanso kapolo. Anaphunzira za M’lungu Kwa Moredekai. Zinthu zinasintha, N’kukhala mfumukazi. Sanakane, anamvera. Nane ndimvere. (KOLASI) Esitere anali Mkazi wolimba mtima. Anamveratu Yehova. N’chitsanzo chabwino. Anadalira M’lungu, Anadalitsidwanso. Nane ndim’tsanzira, Ndidzilimba mtima. 2. Mfumu inkamukonda, Anali wabwino. Anali waulemu, Anali wanzeru. Anatetezatu, Mtundu wake usaphedwe. Sanakane, anamvera. Nane ndimvere. (KOLASI) Esitere anali Mkazi wolimba mtima. Anamveratu Yehova. N’chitsanzo chabwino. Anadalira M’lungu, Anadalitsidwanso. Nane ndim’tsanzira Ndidzilimba mtima. Mukhale wolimba mtima ngati Esitere. Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA Zoti Ana Achite Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Esitere Anali Wolimba Mtima Khalani Bwenzi la Yehova (nyimbo zina) Esitere Anali Wolimba Mtima Chinenero Chamanja cha ku Malawi Esitere Anali Wolimba Mtima https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/501800010/univ/art/501800010_univ_sqr_xl.jpg pkon