NYIMBO 117 Khalidwe la Ubwino Sankhani Zoti Mumvetsere Khalidwe la Ubwino Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (2 Mbiri 6:41) 1. Yehova M’lungu wabwino Mumatidalitsadi. Ndinu wokhulupirika, Mumachita zabwino. Mumasonyeza chifundo Kwa anthu ochimwafe. Tilambire inu nokha. Tikutumikireni. 2. Taona ubwino wanu Mwa atumiki anu. Khalidwe lawo labwino Limatilimbikitsa. Mwatipatsa Mawu anu Ndi abusa abwino. Mutipatse mzimu wanu Tizichita zabwino. 3. Chonde muzitidalitsa Tikachita zabwino. Tikhale okoma mtima Kwa munthu aliyense. M’mabanja ndi mumipingo Ndiponso kulikonse, Muzitithandiza kuti Tizichita zabwino. (Onaninso Sal. 103:10; Maliko 10:18; Agal. 5:22; Aef. 5:9.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Khalidwe la Ubwino IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Khalidwe la Ubwino (Nyimbo 117) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Khalidwe la Ubwino (Nyimbo 117) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016917/sign/wpub/1102016917_sign_sqr_xl.jpg sjj 117