NYIMBO 135 Yehova Akutipempha Kuti: “Mwana Wanga, Khala Wanzeru” Sankhani Zoti Mumvetsere Yehova Akutipempha Kuti: “Mwana Wanga, Khala Wanzeru” Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Onetsani Kaonekedwe ka Mawu Bisani Kaonekedwe ka Mawu Kukula kwa Zilembo Chithunzi (Miyambo 27:11) 1. Mwana wanga undipatse mtima wako. Yemwe akunditonza aone yekha. Ukudziperekadi mofunitsitsa; Anthu adziwe kuti umandikonda. (KOLASI) Mwana wanga wokondedwawe, Khalatu wanzeru chonde. Kutitu unditumikire, Inde mwakufuna kwako. 2. Uzinditumikira mosangalala, Ngakhale ukapunthwa, ndidzakudzutsa. Wina ngakhale angakukhumudwitse, Usadere nkhawa ndidzakhala nawe. (KOLASI) Mwana wanga wokondedwawe, Khalatu wanzeru chonde. Kutitu unditumikire, Inde mwakufuna kwako. (Onaninso Deut. 6:5; Mlal. 11:9; Yes. 41:13.) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Yehova Akutipempha Kuti: “Mwana Wanga, Khala Wanzeru” IMBIRANI YEHOVA MOSANGALALA Yehova Akutipempha Kuti: “Mwana Wanga, Khala Wanzeru” (Nyimbo 135) Chinenero Chamanja cha ku Malawi Yehova Akutipempha Kuti: “Mwana Wanga, Khala Wanzeru” (Nyimbo 135) https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102016935/sign/wpub/1102016935_sign_sqr_xl.jpg sjj 135